Back to Journals
Mphamvu ya umwini ndi Chilolezo
1 min readNewwave Group

Mphamvu ya umwini ndi Chilolezo

guidemusic-industrymalawichichewa

2. Mphamvu ya umwini ndi Chilolezo

Copyright Laws in Malawi

Ku Malawi tili ndi malamulo okhudza mphamvu ya umwini amane anakhazikitsidwa pofuna kuteteza maganizo a anthu a luso. Lamulo la Copyright Act la 2016 ndi limene limatsogolera poteteza mphamvu ya umwini, popereka mphamvu zonse pa ntchito ya munthu wa luso, kwa mwini wake wa luso kwa nthawi yoyikika. (See section A)

Kuloleza nyimbo

Oyimba mu Malawi atha kupeleka chilolezo kuti nyimbo zawo zigwiritsidwe ntchito mosiyanasiyana, monga kulolera kuti nyimbo igwiritsidwe ntchito limodzi powonetsa zinthu zoyenda (pogwitsidwa ntchito muma filimu, zozangalatsa za mu kanema ndi potsatsa malonda) komanso kuziwonetsero za ku gulu(pogwiritsidwa ntchito ku ma konseti, malo omwera mowa, ndi malo ena kumene kumapezeka chigulu). Mgwirizano wa chilolezo umatchula mfundo zopatulika, dipo ndi malamulo ogwiritsira ntchito nyimbo.

Continue reading