Back to Journals
Music Publishing Agreements
1 min readNewwave Group

Music Publishing Agreements

guidemusic-industrymalawichichewa

4. Music Publishing Agreements

Migwirizano yosindikiza ndi kugulitsa imachitika pofuna kuteteza mphamvu ya olemba ndi kupeka nyimbo

Migwirizano yosindikiza ndi kugukitsa

Oyimba ayenera kukhala odekha akamalowa mu migwirizano yosindikiza ndi kugulitsa. Migwirizano imeneyi imafotokoza mwapadera momwe ndalama zidzagawidwire pakati pa munthu wa luso komsanso wosindikiza ndi kugulitsa. Ndikofunikira koposa kuti anthu a luso amvetsetse mawu a mene akugwiritsidwa ntchito kapenanso kufufuza upangiri kwa akatswiri a za malamulo kuti zolinga zawo zikhale zotetezeka.

Protecting Rights

Oyimba akuyenera kuwonetsetsa kuti mphamvu yawo ngati olemba ndi kupeka nyimbo ndi yotetezeka. Kutereku ndi phatikizapo umwinimwini monga wopeka komanso kulandira malipiro oyenerera nyimbo zawo zitagwiritsidwa ntchito.

Chithandizo cha malamulo

Ku Malawi, anthu a luso akhoza kupeza thandizo la ukadaulo kuchokera ku mabungwe monga Malawi Law Society komanso Newwave Group kuti pakhale chilimbikitso chakuti migwirizano yawo ya kusindikiza ndi kugulitsa ikhale yokomera iwowo.

Continue reading