Back to Journals
Kufunika kochulutsa njira zopezera phindu la ndalama
1 min readNewwave Group

Kufunika kochulutsa njira zopezera phindu la ndalama

guidemusic-industrymalawichichewa

1. TKufunika kochulutsa njira zopezera phindu la ndalama

Musicians in Malawi should explore multiple income streams to reduce their reliance on record sales and streaming revenue.

Mavuto a za chuma

Ntchito za oyimba mu Malawi zimakumana ndi zotsamwitsa, kuphatikizapo kulephera kufikira misika ya kunja komanso kujambula nyimbo popanda chilolezo. Kudalira njira zopezera ndalama zodziwika zokha kutha kukhala kovuta kwa anthu a luso.

Ubwino wa kuchulutsa njira

Kuchulutsa njira zopezera chuma, kumathandiza oyimba kuti akhale ndi mpata wopeza njira zopezera ndala zokhazikika makamaka mu nthawi yomwe ma lekodi awo akulidwa mwa apa ndi apo. Kumathandiziranso anthu a luso kutengerapo mwayi wotukula luso lawo komanso ukadaulo mu njira zosiyanasiya.

Continue reading