
Katundu ndi zizindikiro za malonda za padera
2. Katundu ndi zizindikiro za malonda za padera
Merchandise Sales
Anthu oyimba atha kukonza katundu wogulitsa monga malaya okhala ndi chizindikiro chawo,zokongoletsera ndi katundu wina amene anthu angathe kugulidwa kuchokera ku ma konseti, pa matsamba a intaneti komanso mu misika ya kwathu konkuno. Katundu uyu, amathanso kukhala ngati chikumbutso kwa amene amasangalatsidwa ndi ntchito ya oyimba komanso amakhala ngati njira yina yobweretsera ndalama.
Kulenga chizindikiro
Ngati munthu oyimba, kukhala ndi chizindikiro cha mphamvu kumathandizira kukopa anthu osangalitsidwa ndi kutsata oyimba ambiri. Anthu a luso akhoza akhoza kugwiritsa ntchito njira ngati masamba a mchezo a pa intaneti komanso kumanso kuwonekera kwa anthu kuti akhazikitse chithunzithunzi chosankhika komanso kuti athe kumamvana ndi omvera/owatsata mwa kuya.