Back to Journals
Migwirizano ndi migwirizano ya padera ya pakati pa mwini luso ndi ogwiritsa ntchito luso
1 min readNewwave Group

Migwirizano ndi migwirizano ya padera ya pakati pa mwini luso ndi ogwiritsa ntchito luso

guidemusic-industrymalawichichewa

5. Migwirizano ndi migwirizano ya padera ya pakati pa mwini luso ndi ogwiritsa ntchito luso

Migwirizano

Oyimba atha kugwirizana ndi anzawo a luso kapena eni ma kampani, ku Malawi kapenanso kunja kwa Malawi. Migwirizano imeneyi ikhoza kubweretsa ndalama chifukwa chogwirira ntchito mogwirizana, kudziwika ku malo a kutali komanso kupeza anthu kuwonjezekera kwa anthu owatsatira kapena kusangalatsidwa ndi ntchito zawo.

Mgwirizano wa mwini luso kuvomereza munthu wa padera kugwiritsa ntchito luso lake

Kupereka chilolezo kuti nyimbo zigwiritsidwe ntchito mu ma kanema kapena ziwonetsero zina za pa kanema, kunenelera malonda komanso masewero osiyanasiya apa kanema kumatha kubweretsa ndalama. Oyimba atha kugwira ntchito ndi nthambi zopeleka chilolezo kapenanso akonzi kuti athe kupata mwayi woterewo.

Continue reading